Bingu wa Muntharika

From Wikipedia
Jump to: navigation, search
Lula Mutharika

Bingu wa Mutharika, amene anabadwa pa 24 Febuluale 1934, ndi kachenjede wa zachuma (economist), mtsogoleri wa ndale ndiponso Pulezidenti wa dziko la Malawi. A Mutharika anakhala Pulezidenti pa 24 Meyi mchaka ka 2004 pamene anapambana pa chisankho cha Pulezidenti.

Personal tools
Namespaces

Variants
Actions
Navigation
zida
In other languages