Zomba

From Wikipedia
Jump to: navigation, search
View of Zomba plateau from north.JPG

Zomba ndi mzanda omwe uli muchigawo Chakumwera kwa dziko la Malawi.

Mzinda wa Zomba udakhazikitsidwa m'chaka cha 1890 pomwe Angerezi nayamba kulamulira dziko la Malawi (kale ankati Nyasaland). Zomba anali likulu la ulamuliro wa chitsamunda cha Angerezi ku Malawi mpaka pameneko, musogoleri oyamba wa fuko la Malawi a Dokotala Hastings Kamuzu Banda, anasamusa likulu la Malawi kupita ku Lilongwe. Likulu la asilikali a Malawi liri ku Zomba. Nyumba yamalamulo yakhali ili ku Zomba nthawi yaitali mpaka pamene musogoleri Bakili Muluzi anaisamusira ku Lilongwe.