Jump to content

Brunei

From Wikipedia

Brunei (Malay: Negara Brunei Darussalam) ndi dziko lomwe limapezeka ku Asia. Chiwerengero cha anthu: 415.717 (2013).

Bandar Seri Begawan ndi boma lina la dziko la Brunei.