Template:Tsamba Lalikulu/Za Wikipedia
Appearance
Za Wikipedia
- Wikipedia ya Chichewa ndi buku laulere. Ndi wiki, mtundu wa webusaiti yomwe anthu ambiri amawalemba. Izi zikutanthawuza kuti aliyense angathe kusintha tsamba lirilonse podalira pa "kusintha tsamba lino". Mungathe kuchita izi pa tsamba lirilonse losatetezedwa. Mukhoza kuona ngati tsambalo liri kutetezedwa chifukwa lidzati "View source" mmalo mwa "Sintha".
- Pali nkhani 1,099 pa Wikipedia ya Chichewa. Masamba onse ndi omasuka kugwiritsa ntchito. Zonse zafalitsidwa pansi pa Creative Commons Attribution / Share-Alike License 4.0 ndi GNU Free Documentation License. Mungathe kuthandiza pano! Mungasinthe masamba awa ndikupanga masamba atsopano. Werengani masamba othandizira ndi masamba ena abwino kuti mudziwe kulemba masamba apa. Ngati mukufuna thandizo, mukhoza kufunsa mafunso pachithumo cha Community.
Mukamalemba nkhani apa
- Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
- Osagwilitsa ntchito makina ngati google translator! Nkhani yolembedwa pogwilitsa ntchito translator wina aliyense siikhala yomveka bwino (Don't use machine translations!). Nkhani zotelo zizafufutidwa pano mopanda kudziwitsa olembayo komanso kupitiliza kutelo n'kuphwanya malamulo a Wikipediya.
- Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchito pangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
- Khalani wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.