Tsamba Lalikulu/Ntchito zina za Wikimedia
Appearance
| Tsambali ndi gawo la Tsamba Lalikulu ndipo liyenera kukhala lotetezedwa |
Wikipedia imayang'aniridwa ndi Wikimedia Foundation, bungwe lopanda phindu lomwe limakhalanso ndi mapulojekiti:
| Commons Malo omwe aliyense angapeze ndikugawana zithunzi, makanema, ndi mawu aulere. |
Wikifunctions Malo omwe mungapeze ndikugwiritsa ntchito zida zothandiza ndi njira zazifupi pantchito zosiyanasiyana. |
Wikidata Malo omwe chidziwitso chimakonzedwa ndikusungidwa m'njira yoti aliyense azitha kuzipeza ndikuzigwiritsa ntchito momasuka. | |||
| Wikispecies Mndandanda wa nyama zosiyanasiyana, zomera, ndi zamoyo zina. |
Wikipedia Buku lalikulu lapaintaneti lodzaza ndi zambiri zolembedwa mchingerezi zomwe aliyense angaziwerenge ndikuwongolera. |
Wikiquote Malo omwe mungapezeko mawu otchuka komanso osangalatsa ochokera kwa anthu. | |||
| Wikinews Nkhani zomwe aliyense angathe kuziwerenga, kugawana, ndi kuthandiza kulemba. |
Wiktionary Dictionary and thesaurus |
Wikiversity Zida zaulere monga mabuku, makanema, ndi maupangiri omwe amakuthandizani kuphunzira zinthu zatsopano. | |||
| Wikibooks Malo omwe mungapeze mabuku ndi malangizo okuthandizani kuphunzira, ndipo ndi omasuka kugwiritsa ntchito. |
Wikisource Laibulale komwe mungapeze mabuku, zithunzi, ndi zinthu zina zaulere kuti aliyense azigwiritsa ntchito. |
MediaWiki Malo omwe anthu amagwira ntchito popanga ndi kukonza mapulogalamu omwe amayendetsa Wikipedia ndi mawebusayiti ena a Wiki. | |||
| Meta-Wiki Malo oti anthu ogwira ntchito pa Wikipedia ndi ma projekiti ena akonzekere, kukonza, ndi kugwirira ntchito limodzi. |
Wikivoyage Upangiri waulere womwe umakuthandizani kuti muphunzire za malo omwe mungayendere, zinthu zoti muchite, komanso momwe mungayendere. |
Onaninso masamba a Wikimedia Foundation Governance wiki, nawonso.