Tsamba Lalikulu

From Wikipedia
Revision as of 11:35, 4 Apulo 2019 by Thuvack (nkhani | contribs)

Mwalandilidwa ku Wikipedia,

encyclopedia yaulere imene alionse anga thandizeni kukula,

Pakali pano tili 1,028 nkhani mu Chi-chewa zinenero zomwe zimalankhulidwa ku Malawi ndi Zambia.

Mutha kutitsatira pa twitter

Za Wikipedia

  • Wikipedia ya Chichewa ndi buku laulere. Ndi wiki, mtundu wa webusaiti yomwe anthu ambiri amawalemba. Izi zikutanthawuza kuti aliyense angathe kusintha tsamba lirilonse podalira pa "kusintha tsamba lino". Mungathe kuchita izi pa tsamba lirilonse losatetezedwa. Mukhoza kuona ngati tsambalo liri kutetezedwa chifukwa lidzati "View source" mmalo mwa "Sintha".

Mukamalemba nkhani apa

  • Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
  • Osagwilitsa ntchito makina ngati google translator! Nkhani yolembedwa pogwilitsa ntchito translator wina aliyense siikhala yomveka bwino (Don't use machine translations!). Nkhani zotelo zizafufutidwa pano mopanda kudziwitsa olembayo komanso kupitiliza kutelo n'kuphwanya malamulo a Wikipediya.
  • Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchito pangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
  • Khalani wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.

Mu nkhani

Chithunzi chowonetsedwa (Yang'anirani mochedwa kwa lero.)




Tasmanian devil (Sarcophilus harrisii) ndi marsupial odyetsa omwe amapezeka kuthengo kokha ku chilumba cha Australia cha Tasmania. Zimadziwika ndi zomangamanga ndi zomangirira, ubweya wakuda, fungo la phokoso, mokweza kwambiri komanso kusokoneza, kumveka bwino, komanso kupweteka pamene akudyetsa. Mutu wake ndi khosi lalikulu zimalola kuti kuluma kwakukulu kwambiri pa thupi lonse la nyama iliyonse.

Chithunzi: JJ Harrison