User talk:Line dexterman
Add topicDzina langa ndi Dexter line,ninabadwa mchaka cha 1989 mfumu yaikulu Chindi[TA] m'boma la Mzimba. Ndaphunzira m'masukulu ambiri mbiri a boma komanso a private kuchoka mchaka cha 1995 mpakana 2012. Masomphenya anga mumoyo wanga ndimafuna ntadzakhala oyimba m'mene aliri o yimba ena aku Malawi komanso maiko ena.. Ndimachoka mbanja la ana 9 ,kukhala wa chi 6 amuna 5 akazi 4. Mbiri yanga ikupitilira koma kwasopano tilekeze pompa ...ofuna kuziwa zambiri za ine akhoza kundipedza pa EMAIL:Dextermasingi@gmail.com
FACEBOOK:Lin DMAN
TWITTER:@Dmasingi
zikomo.--lin 16:13, 7 September 2012 (UTC) [[]]
Start a discussion with Line dexterman
Talk pages are where people discuss how to make content on Wikipedia the best that it can be. Start a new discussion to connect and collaborate with Line dexterman. What you say here will be public for others to see.