Wikipedia mu Chewa
Jump to navigation
Jump to search
Chi-Chewa Wikipedia ndi kope la Wikipedia mu chinenelo cha Chichewa (Chinyanja). Tsambali limayendtsedwa ndi Wikimedia Foundation ndipo idayambika pa 9 May 2007. Lili ndi zifukwa zoposa 919 monga lero.