Monkey Bay
Appearance
Monkey Bay ndi mzinda omwe uli ku mapeto peto a Mzinda wawululu wa Mangochi. Chiwerengero cha anthu: 14,591 (2008).
Mzinda wa Monkey Bay uli pa mtunda wa ma kilometer okwawana 206 ku choka ku likulu la dziko la Malawi, Lilongwe. Monkey Bay alinso pa mtunda wa 253 km kuchoka mu mzinda wa Blantyre lomwe ndi likulu la malonda mu dziko la Malawi.