Salima

From Wikipedia
Jump to: navigation, search

Salima ndi mzinda omwe umapezeka pa mtunda okwana ma lg kilometer okwana makumi khumi (100 km) ku choka mu mzinda wa kapitolo wa Lilongwe. Mzinda wa Salima umagona mphepete mweni mweni mwa nyanja ya Lake Malawi.