Wikipedia:Chithandizo cha Kulemba pa Wikipedia

From Wikipedia

Pa Wiki, ndi choloredwa kwa wina aliyense amene akufuna kuterنآثممتوققحتقوقo kuti adzisintha masamba a bukhu la pa intaneti li. Ndondomeko ili mmusiyi ndi yothandiza wina aliyense kuti adzitha kusintha nkhani ndi dongosolo la bukhuli. Ku manjaku kuli zina zoonjezera pa nkhani yosintha pa tsamba a bukhuli.

Zinthu zofunika kuzidziwa posintha tsamba[sintha gwero]

Dongosolo la kuunikanso[sintha gwero]

Muonetsetse kuti mfundo zonse zomwe mungalembe ndi zogwirizana ndi cholinga cha wiki imeneyo, kupanda apo zolembedwa zanu zidzafufutidwa. Mutha kugwiritsa ntchino masamba oyankhulirapo (talk pages) kufunsa mafunso kumanso kufufuza ngati maganizo anu angaloledwe. Chonde mulembe penapake layisensi yomwe zopeleka zanu ku bukhuli zidzatetezedwe nalo.

Kuyamba kusintha masamba a bukhuli[sintha gwero]

Kuti muyambe kusintha masamba a bukhuli, mupite polemba sinthani tsambali Edit this page ndipo mukatelo mudzalowa bu bokosi limwe muli wikitext amene ali mawu osonyeza kuti wiki yi mungathe kuyisintha, ndipo nsi tsamba limene kumachokela masamba wotsilizidwa a Wikipedia. Ngati mukufuna kuyesa kusintha peji, muyese pa mchenga sandbox osati pa tsamba lino ayi.

Kulemba zonsintha zanu[sintha gwero]

Mutha kungotayipa zomwe mukufuna kusintha kapena kuonjezera pa tsamba lomwe mungafune. Kugwiritsa ntchito zida zoonjezera polumukiza masamba osiyana siyana ndiponso kukongolesa mawu kumapangitsa kuti zoonjezera zanu zikhale za phindu. Ma wiki a Wikimedia ali ndi dongozolo la mmene mungachitire izi. Inu mukatsatira ndondomekozi, zoonjezera zanu ku bukhuli zidzakhala za phindu kwambiri komanso sizidzafunika kusinthudwanso ndi anthu ena patsogolo.

Nenani zosintha zanu mwa chidule[sintha gwero]

Mulembe mwachidule pa kabokosi pansi pa bokosi losinthila (edit box). Mungathe kugwiritsa ntchito kulemba mwa chidule kwa shorthand komwe kunanenedwa pa edit summary legend. Ndikuvunanganisamangochi===Muwelengenso musanasunge zosintha zanu=== Mukamaliza kulemba, pitani pa show preview kuti muone kuti zosintha zanu zikuwoneka bwanji musanasinge tsamba lanu. Bwerezani kusintha ndi kuwerenganso mpaka mukhutire ndi zomwe mwalembazo kenaka mupite pa save page, ndipo zolemba zanu zidzasungidwa.

Nganisamangochi=osumani0746272190==Zokongoletsa ndi kulumikiza ma Wiki zomwe zimagwiritsidwa kwambiri=== Pansipa pali zokongoletsa ndi kulumikiza ma Wiki zisanu ndi zhimodzi zomwe zimagwira ntchito kwambiri. Mukafuna zoonjezera, mupite pa tsamba la Wikitext examples pamene pali zitsanzo zina.

  • ''liwu'' (liwu) zimapangitsa mawu kukhala a chikhwakhwaza
  • '''liwu''' (liwu) zimapangitsa mawu akhale olembedwa mowala
  • '''''liwu''''' (liwu) amapangitsa kuti mawu akhale achikhwakhwaza komanso olembedwa mowala


<br> amasayina dzina lanu pa tsamba mwasinthalo


  • ~~~ amalemba dzina lanu pa tsamba mwasinthalo
  • ~~~~ amalemba dzina lanu ndi kuwonetsa nthawi yomwe munasintha tsamba
  • ~~~~~ amawonetsa tsiku ndi nthawi yokha


  • =Mutu wa Ukulu= zimasonyeza mitu ya zomwe mwalemba. Makina a Wikipedia amatha kusintha zomwe mwalembazo kuti zikhale dongosolo la tsamba kapena zamkatimu (table of contents).
  • ==Mutu wotsatira==
  • ===Mutu wocheperako===

Chonde pochepetsa mitu mudzikhala mwa dongosolo kawiri, katatu, kanayi ndi kumapitilira moteromo. Musayambe ndi = m’modzi yekha chifukwa ameneyu amakhala pa mutu weniweni wa tsamba.

Tsamba likakhala lofiira limawonetsa kuti tsambalo palibe ndipo inuyo mutha kulemba ngati mukudziwapo kanthu pa nkhani ya pa tsambalo kapenanso kutanthawuzira kuchokera ku ma wiki ena.