Wikipedia mu Chichewa
(Redirected from Wikipedia ya Chewa)

Chi-Chewa Wikipedia ndi kope la Wikipedia mu chinenelo cha Chichewa (Chinyanja). Tsambali limayendtsedwa ndi Wikimedia Foundation ndipo idayambika pa 9 May 2007. Lili ndi zifukwa zoposa 1,023 monga lero.