User talk:Alexander maluza

Page contents not supported in other languages.
From Wikipedia
Takulandirani ku Wikipedia ya Chichewa, Alexander maluza!

Timakonda kukhala ndi anthu atsopano omwe akuthandizira ku Wikipedia.

Chonde musazengereze kufunsa mafunso kwa ogwiritsa ntchito ena othandiza.

Chonde musati muyike mafayilo ku Wikipedia pokhapokha pali chifukwa chapadera chochitira; ntchito pa Wikimedia Commons m'malo mwake.

Tikukhulupirira kuti mudzasangalala ndi nthawi imene mumakhala pano!

Mukhoza kulemba mauthenga anu~~~~.

Lycaon 12:01, 19 March 2010 (UTC)

Ife a wikipedia timakonda ku khala ndi alembi atsopano.

Chonde osazengeleza ngati pali mafunso ofunsa alembi ena omwe amalembera page ya wikipedia ya m'mchinyanga/Chichewa.