Akhristadelfia
Christadelphian Hall in Bath, United Kingdom
Akhristadelfia (chiNgerezi Christadelphians, "abale mwa Khristu") ndi mpingo womwe udakhazikitsidwa m'chaka cha 1848.[1] Chiphunzitso chokana Utatu wa Mulungu pokhulupiria kuti Yesu Kristu ndi Mzimu Woyera si Mulungu.[2]