Biên Hòa

From Wikipedia
Bien Hoa

Bien Hoa dziko Dong Nai ndi tauni yomwe yili ku mpoto kwa dzilo la Vietnam. Tauniyi, yili ma kilomita 20 kuchoka ku mzinda wa Ho Chi Minh City.

Chiwerengero cha anthu: 1.104.495 (2015)