Chingerezi

From Wikipedia

Ndiponso English ina imalankhulidwa ku dziko la America.Galamala yake imafanana koma mawu ena amasiyana.wachitsanzo ena amst hey dziko lina amati hello. English, pa Chichewa amati Chingerezi, ndi chilankhulo cha azungu ochokela ku Britain.