Dasymys incomtus

From Wikipedia
Jump to navigation Jump to search

Dasymys incomtus

Mbewayi imakhala m’malo wokwera koma achinyezi chambiri ndi muudzu. Imadya zomera makamaka mizu kapena mitsitsi, maluwa ndi tizomera tating’onoting’ono. Chifukwa cha ubweya wake wonyankhalala, pena imaoneka ngati Tiri. Pamene mano a Tiri a patsogolo ndi wochekekachekeka, mano a patsogolo a mbewayi yomwe tikunenayi ndi wosalala.