Jump to content

Demokilase

From Wikipedia

Demokilase kuchokera ku chi chingelezi.

Democracy. Ndi ufulu ozilamulira nokha/tokha omwe timauchita potenga nawo gawo mu zochitika za dziko ngati ku votera/kutsankha atsogoleri akuntima kwathu oti ayendetse/kutsogolera dzikoli, ku kuyankhulapo zinthu zikalakwika m'boma ndi zina zambiri