Jump to content

Fodya yamagetsi

From Wikipedia
Photo of device
Fodya wamtundu woyamba ndi ndudu ya fodya yokhala ndi batri yolumikizidwa ndi charger ya USB.

Ndudu yamagetsi (e-cigarette) kapena vape ndi chipangizo chomwe chimatsanzira kusuta fodya. Chimakhala ndi atomizer, gwero lamphamvu monga batri, ndi chidebe monga cartridge kapena thanki. M'malo mosuta utsi, wogwiritsa ntchito amatsokomola nthunzi. [1]

  1. : 674–81. Cite journal requires |journal= (help); Missing or empty |title= (help)