Lazarus Chakwera

From Wikipedia
Lazarus Chakwera

Lazarus McCarthy Chakwera anabadwa pa 5 April 1955 ndipo ndi Malawi yemwe amadziwika bwino ndiza umbusa wa mulungu komanso ndale. Iyeyu anakhalapo wankulu wa mpingo wa Assemblies of God of Malawi kwa zaka zopitilira 20, kufikira chaka cha 2013 pamene anayamba ndale ndipo wakhala president wa dziko la Malawi kuyambira nchaka cha 2020 mu mwezi wa June.