Jump to content

Malamulo olamulira dziko

From Wikipedia

Pa chingelezi"constitution" Mumakhala malamuro akulu akulu adziko omwe amapereka mphanvu ku nthambi zosiyanasiyana za boma kapena anthu wamba, mabungwe osiyana siyana ndi ena ambiri omwe ali mu dziko kutsata malamulo amundzikomo. Mwachitsanzo, mumakhala m'ndandanda wa m'ndondomeko zimene anthu ayenera kutsatira zomwe ndi ndi zofunika kudziko. Mumakhalanso maufulu a wanthu monga mdzika za dziko, uthenga okhudza mmene mthambi za boma ndi zomwe siziri za boma ziyenera ku gwilira ntchito, komanso uthenga okhudza mmene kusamvetsetsa kwa zo chitika za dziko kunga longosoleredwe.