Jump to content

Mtsinje wa Danube

Kuchokera ku Wikipedia
Mtsinje wa Danube

Mtsinje wa Danube ndi mtsinje wa ku Germany, Austria, Slovakia, Hungary, Croatia, Serbia, Romania, Bulgaria, Moldova ndi Ukraine.

Mulitali: 2,860 km.