Mulanje

From Wikipedia
Jump to navigation Jump to search

Mulanje ndi mzinda ku dziko la Malaŵi. Ku Mulanje ndi dera limene kumapezeka phiri lalikulu mu malawi yonse. Phirili ndi lachitatu kukula mu africa yonse.