Mwanza Trial

From Wikipedia
Jump to navigation Jump to search

"Mwanza trial"awa ndi mau amene pachizungu amatanthauza mlandu omwe umaganiziridwa kuti unapalamulidwa ndi a Kamuzu Banda,mtsogoleri woyamba wa dziko la Malawi,John Tembo komanso Mama Kadzamira opha anthu ena omwe anali akulu akulu a boma powachititsa ngozi ku mwanza