Olemba mu ciNyanja

From Wikipedia
Jump to navigation Jump to search

Tsamba lino ndi ndandanda wa alembi amene analembapo ndi kusindikiza chisindikizo (buku) mu ciNyanja (Chichewa).[1]

MaNovelo[edit | sintha gwero]

Mlembi Mutu Mzinda Msindikizi Deti
S J Nthara Nthondo London Religious Tract Society 1934
S J Nthara Nchowa London Longmans 1949
Jerry N Banda Masautso a Kamnjira Lusaka Northern Rhodesia Publishing Bureau 1951
Nelson Chaima Nthano ya Kasimu Lusaka NR and Nyasaland Publishing Bureau 1951
Jackson U Mwale Mkoko Cape Town Longmans 1951
A Mondiwa Mfumu Chilembwe London Longmans 1951
Lester Nkomba Ukawamba London Oxford University Press 1953
C C J Chipinga Zondi Lusaka N. Rhodesia & Nyasaland Joint Publications Bureau 1956
S J Njuweni Kubala Mkumodzi Lusaka N. Rhodesia & Nyasaland Joint Publications Bureau 1957
Henry Kadondo Mtima wa Mfumu Kalanzi London University of London 1958
Josiah E Phiri Kalenga ndi Mnzache Lusaka NECZAM 1958

Za Moyo wa Munthu[edit | sintha gwero]

Mlembi Mutu Mzinda Msindikizi Deti
S J Nthara Namon Katengeza Dedza Nkhoma Synod 1964
S J Nthara Msyamboza Nkhoma Van Wyk Press 1965

Nkhani zosapeka[2][edit | sintha gwero]

Mlembi Mutu Mzinda Msindikizi Deti
S J Nthara Mbiri ya AChewa Dedza Nkhoma Mission Press 1944-45
S J Nthara Mawu Okuluwika M'chinyanja Lusaka Zambia Educational Publishing House 1964
A J Makumbi Maliro ndi Miyambo ya Achewa Blantyre Blantyre Print 1955

Gwero[edit | sintha gwero]

Gwero la ndemanga za mu tsamba lino ndi zisindikizo zotsatirazi:

  1. Chimombo, Prof. Steve, Directory of Malawian Writing, 1992?
  2. S M Made, M V B Mangoche Mbewe and R Jackson, 100 Years of Chichewa in Writing 1875-1975, University of Malawi, Zomba, 1976