Jump to content

Prince Harry, Duke of Sussex

From Wikipedia

Prince Harry, Duke of Sussex (anabadwa pa 15 Seputembala 1984) ndi mwana wa Charles, Prince wa Wales, ndi Diana, Princess of Wales. Iye ali wachisanu ndi chimodzi mzere wotsatizana ku mpando wachifumu wa Britain.