Jump to content

Salima

From Wikipedia

Salima ndi mzinda omwe umapezeka pa mtunda okwana ma lg kilometer okwana makumi khumi (100 km) ku choka mu mzinda wa kapitolo wa Lilongwe.

Mzinda wa Salima umagona mphepete mweni mweni mwa nyanja ya Lake Malawi.

Mzindau mumapezeka anthu a zipembedzo zosiyana-siyana monga Chikhristu achisilamu ndi zina. Anthu ambiri amalankhula Chichewa ndi ena ochepa Chiyao. Chingelezi chimalankhulidwa m`masukulu ndi mzipinda kapena m`malo ogwirira ntchito. Mzindau ndi mlera nkhungwa umene uli ndi nzika zochokera m`mizinda ina ya m`Malawi ndi m`maiko ena.