Wikipedia:Tsamba Lalikulu/Archive 2

From Wikipedia
(Redirected from Tsamba Lalikulu/Archive 2)
Mwalandilidwa ku Wikipedia,
encyclopedia yaulere imene alionse anga thandizeni kukula,
Pakali pano tili 1,028 nkhani mu Chi-chewa zinenero zomwe
zimalankhulidwa ku Malawi ndi Zambia.

Polemba nkhani apa:

  • Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
  • Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchito pangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
  • Khala wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.

Wikipedia mu zitundu zina