Wikipedia:Tsamba Lalikulu/Archive 2
Appearance
Polemba nkhani apa:
- Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
- Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchito pangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
- Khala wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.
Wikipedia mu zitundu zina
Wikipedia iyi yalembedwa mu Chichewa. Kuyambira mu 2001, pakali pano muli nkhani 1,041. Ma Wikipedias ambiri amapezeka; ma Wikipediya ena amu Afrika ali pansipa.
Afrikaans | Luganda | Gĩkũyũ | Hausa | Igbo | KiKongo | Lingala | Kirundi | Ikinyarwanda | chiShona | Sesotho | Sesotho sa leboa | Kiswahili | SiSwati | Xitsonga | Setswana | chiTumbuka | Tshivenda | isiXhosa | Yorùbá |