User talk:Jose77

Page contents not supported in other languages.
From Wikipedia

Hi, please do not impersonate other people (Request for adminship). Lycaon 16:49, 8 May 2007 (UTC)

Ok. Sorry. --Jose77 05:19, 9 May 2007 (UTC)


Takulandirani ku Wikipedia ya Chichewa, Jose77!

Timakonda kukhala ndi anthu atsopano omwe akuthandizira ku Wikipedia.

Chonde musazengereze kufunsa mafunso kwa ogwiritsa ntchito ena othandiza.

Chonde musati muyike mafayilo ku Wikipedia pokhapokha pali chifukwa chapadera chochitira; ntchito pa Wikimedia Commons m'malo mwake.

Tikukhulupirira kuti mudzasangalala ndi nthawi imene mumakhala pano!

Mukhoza kulemba mauthenga anu~~~~.

Lycaon 08:21, 9 May 2007 (UTC)

Translation[sintha gwero]

Hi I will try Thx Ineyo

Translation[sintha gwero]

Kulandila Mzumi Woyera, kumene kumaoneka ndi kulankhula malilime, ndi kumene kumatsimikiza kuti tili ndi mbali ku ufumu wa kumwamba.

Kubatizidwa mmadzi ndi chizindikilo cha kukhululukidwa ku machimo komanso kubadwanso mwa tsopano. Kubatizidwa kotele kumayenera kuchitika pa malo amene pamapezeka madzi a chilengedwe monga pa mtsinje, pa nyanja kapenanso kasupe. Mbatizi, amene analandila kale ubatizo wa madzi ndi wa Mzimu Woyera, ndi amene amabatiza anthu m'zina la Yesu Khristu. Aliyense wobatizidwa amayenera kumizidwiratu mmadzi atawerama mutu ndikuyang'ana nkhope yake pansi.

Dongosolo lotsuka mapazi a anthu limamulola munthu kukhala ndi mbali kwa Yesu Khristu. Limakumbutsanso kuti munthu ayenera kukhala ndi chikondi, chiyero, kudzichepetsa, kukhululuka komanso kugwira ntchito ya Mulungi. Aliyense amene anabatizidwa amayeneranso kutsukidwa mapazi ake mu dzina la Yesu Khiristu. Anthu amathanso kuloledwa kutsukana mapazi.

Mgonero ndi dongosolo lokumbukira imfa ya Ambuye Yesu. Umatilora kuti tikhale ndi mbali pa imfa yake kuti tidzakhale ndi moyo wosatha ndi kudzutsidwa pa tsiku lomaliza. Dongosoloti limachitika pa nthawi ina iliyonse pafupi pafupi ndipo amagwiritsa ntchito mkate opanda chofufumitsa komanso madzi ochokera ku ma grapes okha basi.

Chichewa Wikipedia Interface[sintha gwero]

Main Page = ? Tsamba lalikulu

Community portal = ? Tsamba la anthu wonse

Current events = ? Zomwe zikuchitika padakali pano

Recent changes = ? Kusintha kumene kwachitika posachedwa

Random page = ? Tsamba losankhidwa mopanda dongosolo

Help = ? Chithandizo

Donations = ? Tsamba lopelekelapo chithandizo cha makobili

Navigation = ? M'mene mungapezere zomwe mukufuna

Search = ? Fufuzani

Go = ? Pitani

Toolbox = ? Zida

What links here = ? Masamba olumikizana ndi tsambali

Related changes = ? Kusintha kofanana ndi tsamba lino

Upload file = ? Kulowetsa zomwe munalemba kale

Special pages = ? Masamba apadera

Printable version = ? Tsamba loti mungathe kupulinta

Permanent link = ? Kulumikiza kosachotseka

Cite this article = ? Gwiritsani ntchito tsambali pa malo ena

In other languages = ? Mu zilankhulo zina

Article = ? Tsamba

Discussion = ? Zokambirana

talk = > ZOyankhula

Edit = ? Kusintha tsamba

History = ? Mbiri ya tsamba

Delete = ? Fufutani tsamba

Protect = ? Tetezani tsamba

Log in = ? Lowani

Create Account = ? Tsegulani akaunti

Create an account = ? Tsegulani akaunti

Create article = Lembani tsamba

Not logged in = ? Simunalowe

Log out = ? Tulukani

Move = ? Samutsani

Move page = ? Samutsani tsamba

Move this page = ? Samutsani tsambali

moved to = Linasamukira ku

$1 moved to $2 = $1 linasamukira ku $2

Reason = Chifukwa

Watch = ? Penyani tsambali

My Watchlist = ? Ndondomeko ya masamba amene ndikuwapenyetsetsa

My talk = ? Ndondomeko yanga yoyankhula ndi anthu ena

My preferences = ? Chisankho changa cha mmene masamba aziwonekera

My contributions = ? Zolemba zanga m'bukhuli

Summary = ? Mwa chidule

This is a minor edit = ? Kusintha uku ndi kwa pang'ono

Watch this page = ? Wonetsetsani tsamba ili

Save page = ? Sungani tsamba m'bukhuli

Show preview = ? Onetsani m'mene tsamba lasinthila

Show changes = ? Onetsani zimene zasintha pa tsambali

Cancel = ? Siyani, musasinthenso

Editing Help = ? Chithandizo chosinthila bukhuli

User page = ? Tsamba la iwe mwini

Username = ? Dzina logwiritsa ntchito

Password = ? Liu la chitetezo

Re-type password = ? Lembaninso liu la chitetezo

E-mail = ? Kalata ya pa kompyuta

System messages = ? Mauthenga ochokera mmakina

System messages = ?

Remember my login on this computer = ? Mukumbukire dzina langa pa makinawa

User:Contributions = ? Wogwiritsa ntchito:zosintha

Login required to edit = ? Kulowa kdi kofunika kuti tsambali lisinthidwe

View source = ? Kuona kumene tsambali lachokera

new messages = ? Mauthenga atsopano

You have new messages on $1 = ? Muli ndi mauthenga atsopano


== Welcome, $1! == Your account has been created. Don't forget to change your Wikipedia preferences. = ? ==Mwalandiridwa, $1!== Akaunti yanu ya Wikipedia tsopano yatsegulidwa. Chonde musayiwale kusintha m'mene mukufuna kuti masamba anu adziwonekera.

January Januale

February Febuluale

March Malichi

April Epulo

May Meyi

June Juni

July Julaye

August Ogasiti

September Sepitembala

October Okotobala

November Novembala

December Disembala

Sunday Lasabata

Monday Lolemba

Tuesday Lachiwiri

Wednesday Lachitatu

Thursday Lachinayi

Friday Lachisanu

Saturday Loweruka

Disclaimers Zomwe bukuli silidzakhala nazo ndi mulandu

Privacy Policy Malamulo okhudza chinsinsi cha zolembedwa m'bukhuli

About Wikipedia Zokhudza Wikipedia

Adminship[sintha gwero]

For now I'd rather just translate the articles, but thanks for your nomination. By the way, I'm a she, not a he :-D Ineyo 08:48, 17 May 2007 (UTC)

Your account will be renamed[sintha gwero]

04:22, 18 March 2015 (UTC)