Vano Merabishvili

From Wikipedia
Jump to navigation Jump to search
Vano Merabishvili

Ivane "Vano" Merabishvili (Chijojiya: ივანე [ვანო] მერაბიშვილი; wobadwa pa 15 Epulo 1968) ndi wandale waku Georgia. Adakhala Prime Minister waku Georgia pa 4 Julayi 2012. Nthawi yake idatha atasiya ntchito pa 25 Okutobala 2012.

Zolemba[Sinthani | sintha gwero]