Jump to content

Wikidata

From Wikipedia

Wikidata ndi wiki yomwe ndi mndandanda wa data pa intaneti. Zomwe zimasungidwa ku Wikidata zingagwiritsidwe ntchito ndi mawebusaiti othandizana monga Wikipedia. Wikidata yapangidwa kuti anthu ndi makina athe kuziwerenga. Kuyambira mu September 2016, ili ndi zinthu zoposa 20 miliyoni za deta.[1]

References[Sinthani | sintha gwero]

  1. "Statistics". Wikidata. Wikimedia Foundation. September 5, 2016. Retrieved September 5, 2016.