Jump to content

Wikipedia:Tsamba Lalikulu/Archive 3

From Wikipedia
Mwalandilidwa ku Wikipedia,
encyclopedia yaulere imene alionse anga thandizeni kukula,
Pakali pano tili 1,041 nkhani mu Chi-chewa zinenero zomwe
zimalankhulidwa ku Malawi ndi Zambia.

Polemba nkhani apa:

  • Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
  • Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchito pangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
  • Khala wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.

Chithunzi chowonetsedwa 




Mitundu ya Sprekelia formosissima, mitundu yofala kwambiri ya zomera za Sprekelia zomwe zimapezeka ku Central America, koma zimakula padziko lonse lapansi. Sprekelia amatchedwa "Aztec maluwa", ngakhale kuti si maluŵa enieni.

Chithunzi: Noodle snacks


Wikipedia mu zitundu zina