Jump to content

Wolembedwa ndi Yohane

From Wikipedia
  1. Pachiyambi pa zonse Iye amene amatchedwa dzina loti Mawu, analipo kale. Anali kwa Mulungu, Edipo anali Mulungu.
  2. Anali kwa Mulungu chiyambire.
  3. Mulungu analenga zonse ndi lye, Edipo popanda Iye sanalenge kanthu kalikonse.
  4. Mwa Iyeyo munali moyo, Edipo moyowo unalikuŵalira anthu.
  5. Kuŵalako kulikuunikabe mandita, Edipo nyima unalephera kugonjetsa kuŵalako.
  6. Mulungu anatema munthu wina, dzina lake Yohanne.
  7. Iye anabwera kudzachitira umboni wakewo.
  8. Si kuti iyeyo anali kuŵalako ayi, koma anangobwera kudzachitira umboni kuŵalako.
  9. Kuŵala kwenikweni, kounikira anthu onse, kunalikudza pansi pano.
  10. Mawuwo anali n’dzino lapansi, Edipo Mulungu analenga dziko lapansi ndi Iye, komabe anthu a pansi pano sanamzindikire.