Archie Mountbatten-Windsor

From Wikipedia

Archie Harrison Mountbatten-Windsor (anabadwa pa 6 Meyi 2019) ndi mwana wa Prince Harry, Duke wa Sussex, ndi Meghan, Duchess wa Sussex. Iye ali wachisanu ndi chiwiri mzere wotsatizana ku mpando wachifumu wa Britain.