Muslim

From Wikipedia

Anthu omwe amatchedwa Muslim amakhulupirira 'Allah' ndi mneneri 'Muhammad'. Asilamu amawerenga 'Koran' ngati buku loyera.