Jump to content

Turkey

From Wikipedia

Turkey (tursk: Türkiye) ndi dziko lomwe limapezeka ku Europu & Asia. Istanbul ndi boma lina la dziko la Turkey. Dzikoli linayandikana ndi Greece cha ku madzulo, Gergiomo cha ku mpoto ndi Iran, Armenyomo, Azerbaijan kuzungulira kum’mawa, kummwera ndi ku madzulo.

Chiwerengero cha anthu: 79 463 663 (2016).